Bladder Cancer Message from One Community
Mwezi wa May unali mwezi wokumbukira za Matenda a khansa ya m’chikodzodzo. One Community MW mogwirizana ndi bungwe la World Bladder Cancer Patient Coalition akhala akudziwitsa anthu za matendawa kudzera mu njira zosiyanasiyana. Bambo Wisdom Nyirenda, omwe ndi mkulu wowona…